Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

107. Nthano Ya Yesu Uzeni

TELL ME THE STORY OF JESUS

TELL ME THE STORY OF JESUS

1. Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu;
Nthano yodala uzeni, Nthano yoposa zonse.
Nyimbo ya ’ngelo uzeni, Nthawi yobadwa Yesu,
Ulemelero kwa Mlungu, Ndipo mtendere pano.

*CHORUS:
Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu,
Nthano yodala uzeni, Nthano yoposa zonse.*

2. Nena masiku ajawo, Mbuye nasala kudya,
Anayesedwa koopsa, Koma analakika.
Za ntchito yake uzeni, Ndi za zisoni zake,
Anazunzidwa kolimba, Mphawi wopanda kwao.

3. Za mtanda wake uzeni, Ndi za zowawa zake,
Za manda ake uzeni, Ndi za kuuka kwake.
M’nthano ndiona chikondi, Cha Yesu, Mbuye wanga,
Mmene ndiimva ndilira, Anawombola ine.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 107

Permanent page: number and title URL

This page preserves Nthano Ya Yesu Uzeni as Hymn 107 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.