Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

124. Ndikweze Yesu Yekha

NOT I, BUT CHRIST

NOT I, BUT CHRIST

1. Ndikweze Yesu yekha m’zinthu zonse;
Amveke, aoneke yekhayo;
Mu ntchito, m’maganizo ndipo m’mau,
Ambuye aoneke yekhayo.

2. Ndi Yesu atonthoza akulira,
Yekhayo angachotse msoziwo;
Yekhayo angatule akatundu,
Yekhayo angachotse manthawo.

3. Ndileke mau onse ena chabe,
Ndileke zakupusa zangazo;
Ndikweze Yesu, ndisanyade konse,
Ndisadzitame, koma Iyeyo.

4. Ndi Khristu amapatsa ’ne zosowa.
Ndi yekha amapatsa mphamvunso.
Yekhayo m’thupi , m’moyo, ndi mu mzimu;
Ndi Khristu yekha nthawi zonsezo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 124

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndikweze Yesu Yekha as Hymn 124 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.