Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
146. Mukhale M’mtima Mwanga
THY LIFE WITHIN ME
THY LIFE WITHIN ME
1. Mukhale m’mtima mwanga Ee, Yesu, Mfumuyo.
Mundiyankhire ine Mafunso angawo.
Mukhale m’mtima mwanga, Mnditsogoleretu,
Kuti ndionetsere Ukulu wanuwo.
2. Kachisi wa mtimanga Wayeretsedwatu,
Ulemelero wanu Uwale mkatimo;
Ndi thupi langa lonse Likhale lanulo,
Lichite nthawi zonse Kufuna kwanuko.
3. Ziwalo zanga zonse, Mzilamuliretu,
Muchite nazo zonse Kufuna kwanuko;
Ndidzipereke ndense, Osang’ung’udzanso,
Polamulidwa nanu Mu ntchito zangazo.
4. Ndidzapumula ndithu Mu mtima mwangamo,
Ndidzalindira Inu, Mukandifunatu;
Mukhale m’mtima mwanga, Ee, Yesu, Mfumuyo,
Mundiyankhire ine, Mafunso angawo.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 146
Permanent page: number and title URL
This page preserves Mukhale M’mtima Mwanga as Hymn 146 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.