Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

150. Okunkhawo Ali Kuti?

WHERE ARE THE REAPERS?

WHERE ARE THE REAPERS?

1. Okunkhawo alitu kutiko?
Amene akunkhatu zabwino?
Kuchoka mu dziko loipali,
Pochita ndi mau a Mlunguyo?

*CHORUS:
Ndanitu adze kudzakunkha,
Kusonkhanitsira anthu m’mwambamo?
Ndi yani atithandizeko,
Pofunafuna zobalazo?*

2. Pitani mu mphambano monsemo,
Funani mupezemo abwino;
Pitani kwa anthu ponse ponse,
Musonkhanitsire kumwambako.

3. Zobala zakhwima ponse ponse,
Za m’dzikomu zilindira ife.
Okunkha achepa ku ntchitoyi,
Zambiri zidzaonongekatu.

4. Anthuni idzani ndi zidazo,
Kudzasonkhanitsa za m’mundamo;
Gwiranibe mpaka Ambuyeyo,
Adzabwera ali kukondwatu.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 150

Permanent page: number and title URL

This page preserves Okunkhawo Ali Kuti? as Hymn 150 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.