Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

152. Yesu Mundilankhule

SPEAK TO MY SOUL

SPEAK TO MY SOUL

1. Yesu, mundilankhule, Mau ofatsawo;
Mndinong’oneze kuti, Sulitu wekha ’we.
Mtima munditsegule, Kuti ndimvere ’Nu;
Mdzaze mu mtima mwanga, Kuti ndikondwedi.

*CHORUS:
Mundinong’onezetu, Mwa nsisi zanuzo,
Udzagonjetsa ndithu, Udzamasukadi.
Mundilankhule, Mbuye, Tsiku ndi tsikunso,
Ndimvetu mau anu, Sulitu wekha ’we.
*

2. Yesu, munene mau Ndi ana anuwo,
Kuyang’anira Inu, Muwaphunzitsetu;
Kuti apereketu Moyo kwa Inuyo,
Udze ufumu wanu, Kuti ’dzaone ’Nu.

3. Kale munaonetsa Kufuna kwanuko,
Yanga ndidziwe ntchito, Ndichite zanuzo;
Ndilemekeze Inu, Kwa anthu onsewo,
Nchite kufuna kwanu, Masiku onsewo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 152

Permanent page: number and title URL

This page preserves Yesu Mundilankhule as Hymn 152 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.