Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
163. ’Mvani Yesu Aitana
HERE AM I, SEND ME
HERE AM I, SEND ME
1. ’Mvani Yesu aitana, Ndani angagwiretu?
Mindayo yayera kale, Ndani akakunkhemo?
Momvekadi aitana, Mphotho ’dzalandira ’we.
Ndani angayankhe msanga, Ndine Mbuye, tumeni.
2. Nkana sungapite mtali Ku maiko enawo,
Ungapeze anthu ena Apafupi ndi iwe.
Ngati sungalalikire Monga ngati Paulo,
Unganene za chikondi Cha Ambuye wakoyo.
3. Ngati sungakhale mlonda Wochenjeza anthuwo;
Kuwauza anthu njira Yonka nayo mmwambamo;
Pakupempherera ena, Ungagwire ntchitoyo.
Ungachite ngati Huri Pothangata Moseyo.
4. Mmene anthu alikufa, Mbuye aitanabe;
Wina asamamve nuti, Singachite kanthui.
Gwira ntchito wakupatsa, Nuigwire msangatu;
Ndi kuyankha poitana, Ndine Mbuye, tumeni.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 163
Permanent page: number and title URL
This page preserves ’Mvani Yesu Aitana as Hymn 163 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.