Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
178. Mmamawa Kapena Potuluka Dzuwa
CHRIST RETURNETH
CHRIST RETURNETH
1. Mmamawa kapena potuluka dzuwa,
Ambuye Yesuyo ’dzafika ndi mphamvu,
Ndi ulemerero wo’kulu kutenga
Anthu ake mu dzikoli.
*CHORUS:
Yesu, Mbuye wathu,
’Dzayimba mokondwa liti?
Khristu adza, Khristu adza,
Aleluya amen. Aleluya amen.*
2. Kapena usana kapena madzulo,
Kapena usiku pamene Ambuye
’Dzafika mu ulemelero kutenga
Anthu ake mu dzikoli.
3. Tidzakondwa ngati tidzanka osafa,
Opanda kudwala, chisoni, maliro;
Kungokhwathulidwa podzadza kutenga
Anthu ake mu dzikoli.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 178
Permanent page: number and title URL
This page preserves Mmamawa Kapena Potuluka Dzuwa as Hymn 178 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.