Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
180. Sitidziwa Nthawi Ya Kudza
WE KNOW NOT THE HOUR
WE KNOW NOT THE HOUR
1. Sitidziwa nthawi yakudza kwa Mbuye,
Koma zooneka pa dziko zinena
Adzabwera msanga, tikondwa,
Komatu sitidziwa nthawi.
*CHORUS:
Adzatu! Tikonzeke, tilinde!
Adzatu! Aleluya! Aleluya!
Adza ndi mphamvu za ’Tate wake,
Komatu sitidziwa nthawi.*
2. Ku’nika kulipo kwa anthu a nzeru,
Cho’nadi chilipo mu mau a Mlungu,
Alembi anena momveka,
Komatu sitidziwa nthawi.
3. Tilinde, tipemphe ndi nyali zowala,
Tigwirenso ntchito mpakatu abwera.
Poona zozizwa tiyimbe,
Komatu sitidziwa nthawi.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 180
Permanent page: number and title URL
This page preserves Sitidziwa Nthawi Ya Kudza as Hymn 180 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.