Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

19. Akristu Tiyeni

ONWARD, CHRISTIAN SOLDIERS!

ONWARD, CHRISTIAN SOLDIERS!

1. Akhristu tiyeni! Nkhondo tigwire,
Yesu Mbuye wathu, Atitsogoza,
Ona mbuye yekha, Atithandiza;
Ndi mbendera yake, Tiyitsatira.

*CHORUS:
Akristu tiyeni! Nkhondo tigwire,
Yesu Mbuye wathu, Atitsogoza.

*2. Nkhondo ya Satana, Msanga ithawa,
Akristu tiyeni, Tidzapambana;
Mphamvu zake zitha, Yesu titama;
Yimbani anzathu Nyimbo tikweza.

3. Gulu lalikulu, Adza Akhristu;
Titsatana nawo, Ana a Mlungu;
Sitipatukana, Tonse tikhala,
Ndi mtima umodzi, Timakondana.

4. Zonse za pa dziko, Zidzatheratu;
Koma mpingo wake, Ukhalitsabe;
Mphamvu ya Satana, Idzalefuka;
Yesu nalonjeza Ndidzalimbitsa.

5. Idzani Akhristu, Kutithandiza,
Nyimbo za Mulungu, Tidzayimbitsa;
Khristu ayenera, Ndiye Mfumuyo,
Tidzamlemekeza, Nthawi zonsezo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 19

Permanent page: number and title URL

This page preserves Akristu Tiyeni as Hymn 19 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.