Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

199. Ulemu Kwa Mulungu

TO GOD BE THE GLORY

TO GOD BE THE GLORY

1. Ulemu kwa Mlungu, Ambuye wathu,
Akonda, napatsa ’fe Mwana Wake;
Napatsatu moyo kuombola ’fe,
Pa khomo la moyo natsegulatu.

*CHORUS:
Tamani Mbuyeyo, Dziko limvere ’Ye;
Tamani Mbuyeyo, Anthu akondwetu;
Idzani kwa ’Tate mwa Mwana Wake,
Mpatseni ulemu anakonda ’fe.*

2. Anapulumutsa ndi mwazi Wake
Amene akhulupirira mwa ’Ye.
Ngakhale wochimwa koposa ndithu,
Adzakhululukidwa mwa Yesuyo.

3. Anatiphunzitsa zopambanazo,
Tikondwa mwa Yesu, Ambuye wathu;
Komabe ’dzazizwa kopambanadi,
Pamene atenga ’fe, kumwambako.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 199

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ulemu Kwa Mulungu as Hymn 199 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.