Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
203. Nkhoswe Yadza
THE COMFORTER HAS COME
THE COMFORTER HAS COME
1. Lalikira mau konse kuli anthu
A mtima wosowa A m’dziko latsoka,
Mkhristu ali yense Anene mokondwa
Nkhoswe yafikadid!
* CHORUS:
Nkhoswe yafikadi, Nkhoswe yafikadi!
Mzimu wa Mulungu pangano la Mbuye;
Lalikira mau Konse kuli anthu,
Nkhoswe yafikadi!
*
2. Usiku wapiti, Kunja nako kwaca;
Kulira kwaleka, Ndi mkwiyo naonse,
Pamapiri napo Dzuwa lioneka;
Nkhoswe yafikadi!
3. Mfumu ya mafumu ibwera ndi mwayi,
Kwa ocimwa onse Kudzapulumutsa;
M’malomo mwa cete Mumveka nyimbo
Nkhoswe yafikadi!
4. Cikondi cakuya Ndicimene bwanji,
Kwa anthu ocimwa Apeze cisomo, Wocimwa ngati’ne Ndingawale bwanji;
Nkhoswe yafikadi!
5. Kuyimba kumveke Mlengalenga monse;
Oyera a m’mwamba Ndi a pansi pano
Abvomerezane Nyimbo yacikondi,
Nkhoswe yafikadi!
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 203
Permanent page: number and title URL
This page preserves Nkhoswe Yadza as Hymn 203 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.