Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

237. Akristu Limbikani!

STAND UP! STAND UP FOR JESUS!

STAND UP! STAND UP FOR JESUS!

1. Akristu limbikani, imani mtimanji!
Mbendera nyamulani, musanthenthemerebi.
Wotsogolera wathu ndi Mwana wa Mulungu;
Adzagonjetsa onse, adani athuwo.

2. Tigwire nkhondo yomwe ya Mbuye wathuyo;
Ticotse zakuipa zokhala mtimamo.
Sitikwanira tokha kuleka zinthu zomwe;
Koma Mbuyathu Yesu atithangatatu.

3. Tsopano timenyana ndi zakuipazo,
Pamene nkhondo yatha tidzanka kwathuko;
Yesu adzalandira ankhondo ace onse,
Adzakhalitsa naye Kumwamba komweko.

4. Limbikani anzathu! Msanga nkhondo itha
Lero kuli cinkhondo, mawa tigonjetsa
Kwa iye wolakika, adzakhala moyo;
Pamodzi ndi Mfumuyo ’dzakhala kosatha.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 237

Permanent page: number and title URL

This page preserves Akristu Limbikani! as Hymn 237 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.