Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
241. Dziko Labwino
BEULAH LAND
BEULAH LAND
1. Ndapeza dziko lokoma, Ndi zinthu zonse ndi zanga;
Zokometsetsa konseko, Usiku wandicokera.
* CHORUS:
O, dzikolo, lokomalo, Pa phiri lokometsalo,
Ndipenyetsetsa ku Nyanja, Manyumba andikonzera,
Ndiyang’anitsa dzikolo, Komwe ndidzakhalitsako.
*
2. Ndiyenda ndi Mpulumutsi, Andikondwera m’njiramo;
Anditsogolera bwino, Kumwamba ndikafikeko.
3. Mphepo zinunkhira bwino, Za mitengo ya dzikolo,
Maluwa nao safota, Mitsinje simaumako.
4. Mphepo za kumadzulozo, Ndi nyimbo kumwambako,
Angelo onyezimira Ayimba za mphamvu zace.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 241
Permanent page: number and title URL
This page preserves Dziko Labwino as Hymn 241 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.