Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
245. Palibe Dzina Lina
NO OTHER NAME
NO OTHER NAME
1. Dzina lokhalo la Yesu, Ndilo dzina lokoma;
Likondwetsa ’ngelo m’mwamba, Ndi Akhristu tonsefe.
* CHORUS:
Dzina, dzina, Palibe longa la Yesu,
Dzina, dzina, Palibe longa la Yesu.
*
2. Dzina lokha ndi la Yesu, Pamene ndibvutika;
Dzina lokha ndi la Yesu pamene ndikondwera.
3. Ndikufuna kudzamwona, Podza mu’lemerero,
Ndidzamve Wacita bwino, Ndidzakondwererako.
4. Ngat’ afuna ngwire ntchito, M’munda wace wa mpesa,
Kuli bwino Yesu yekha, ’Dalitse ntchito zanga.
5. Ngat’afuna kuti ndife, Akhudze thupi langa,
Kukhale bwino ndi Yesu, Ndikhulupira mwa’ye.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 245
Permanent page: number and title URL
This page preserves Palibe Dzina Lina as Hymn 245 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.