Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
26. Ndisauka Ndinachimwa
JUST AS I AM
JUST AS I AM
1. Ndisauka ndinachimwa, Koma Inu mwandifera,
Ndipo ndamva mundi’tana, Mwana Mlungu ndingobwera.
2. Ndisauka ndimasowa, Mphamvu ya kuyera mtima,
Mwazi wanu unditsuka; Mwana Mlungu ndingobwera.
3. Ndisauka, sindikhoza Kwiletsa nkhondo mu mtima,
Ndi chisoni, mantha, nkhawa, Mwana Mlungu ndingobwera.
4. Ndisauka sindiona, Ndimadwala ndilefuka,
Zonse ndizitaya kwa ’Nu, Mwana Mlungu ndingobwera.
5. Inde, Yesu mulandira, Muchiritsa mpulumutsa,
Mau anu ndivomera, Mwana Mlungu ndingobwera.
6. Inde, Yesu, mundikonda, Zonse zina ndazitaya,
Tsono kukakhala wanu, Mwana Mlungu ndingobwera.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 26
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ndisauka Ndinachimwa as Hymn 26 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.