Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

288. Anadzatu Kwa Yesu

THEY BROUGHT THEIR GIFTS TO JESUS

THEY BROUGHT THEIR GIFTS TO JESUS

1. Anadzatu kwa Yesu ndi mphatso zaozo,
Ndi Mtima wa cikondi Natula zonsezo
Zokoma Mtima ntchito Zothandizanatu,
Ndi zopereka zao Ndizo za mtengotu.

* CHORUS:
Tulani mphatso zanu kwa Yesu Mbuyeyo
Pereka Mtima wanu Pa guwa lacelo.
*
2. Pakati pa opatsa Naima mlendoyo
Naona anthu ena Napatsa zaozo,
Naye nalakalaka Kupatsa zacezo,
Analibetu kanthu Kopatsa Mbuyeyo.

3. Nalira, Mbuye wanga, Wokoma Mtima ’Nu,
Tengani Mtima wanga Wodzadza chimolo
Ambuye namuyankha Usati yachepa;
Yakoyo, mwana wanga Yaposa zonsezo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 288

Permanent page: number and title URL

This page preserves Anadzatu Kwa Yesu as Hymn 288 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.