Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
3. Maso Ndi Maso
FACE TO FACE
FACE TO FACE
1 Maso ndi maso ndi Khristu, Kodi ndidzachitanji?
Mmene ndidzaona Yesu, Yemwe anandifera.
*CHORUS:
N’dzamona maso ndi maso, Kuseri kwa mitambo;
Posachedwa ndidzamona, Mulemerero wace!
*
2 Tsopano ndimona Iye, Mwa chizimezimetu,
Tsiku lija ndidzaona, Ulemerero wache.
3 Pamene zowawa zonse, Nthenda ndi imfa zitha,
Dziko likadzakonzedwa, Ndidzakondwa koposa!
4 Lodala tsikulo m’mene! Ndidzamuona Yesu,
Mpulumutsi wanga yemwe, Anandikonda ine.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 3
Permanent page: number and title URL
This page preserves Maso Ndi Maso as Hymn 3 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.