Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
310. Ndifuna Kukhala Ndi Yesu
I WANT TO LIVE CLOSER TO JESUS
I WANT TO LIVE CLOSER TO JESUS
1. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Kuyang’ana nkhope yace,
Adzaze mtimanga cisomo cace, Ndifuna kukhala naye.
* CHORUS:
Khala pafupi, mfupi nd Yesu, Pa mbali ya Iyeyo;
Kuyang’ana pa nkhope yabwinoyo, Ndifuna kukhala naye.
*
2. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Kumtsata pafupifupi
Ndi kuti ndimvetse polankhula ’Ye, ponena lonjezo lace.
3. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Pafupi masiku onse
Pogwiratu dzanja la mphamvu yace, Nkalowa m’ufumu wace.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 310
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ndifuna Kukhala Ndi Yesu as Hymn 310 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.