Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
328. NATIONAL ATHEM (Chichewa)
**
**
1. Mlungu dalitsani Malawi,
Mumsunge m’mtendere,
Khonjetsani adani onse,
Njala nthenda nsanje,
Lunzitsani mitima yathu,
Kuti tisaope,
Mdalitse mtsogoleri nafe,
Ndi Mayi Malawi,
2. Malawi dziko lokongola,
Lachonde ndi ufulu,
Nyanja ndi mphepo ya m’mapiri,
Ndithudi tadala,
Zigwa, mapiri, nthaka, Dzinthu
Mphatso zaulere
Nkhalango, madambo abwino
Ngokoma Malawi.
3. O’ Ufulu tigwirizane,
Kukweza Malawi
Ndi chikondi, khama kumvera,
Timutumikire
Pa nkhondo nkana pa mtendere
Cholinga n’chimodzi
Mayi, Bambo, tidzipereke
Pokweza Malawi
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 328
Permanent page: number and title URL
This page preserves NATIONAL ATHEM (Chichewa) as Hymn 328 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.