Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

52. Kasupe Wa Madalitso

COME, THOU FOUNT

COME, THOU FOUNT

1. Idzani ndi madalitso, Mtima wanga uyimbe;
Nsisi zanu zisaleke, Kuti tiyamike ’Nu,
Phunzitseni kumvera ’Nu, Kuti ndikudziweni,
Pamene chiyembekezo Chidzaza mtima wanga.

2. Ndinutu thandizo langa, Mwandifikitsa pano,
Ndipo mwa chifundo chanu Ndikafika kwathuko.
Anandifuna Yesuyo, Posochera mtalimo;
Anakhetsa mwazi wake Kundiombola ine.

3. M’ndipatse chisomo chanu, Pakuti ndichisowa!
Mundikokere kwa Inu Ndi chikondi chanucho.
Sindifuna kusochera, Kukusiyani Inu,
Tengani Mtima wangawu; Ukhale wanu konse

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 52

Permanent page: number and title URL

This page preserves Kasupe Wa Madalitso as Hymn 52 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.