Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

54. Ndifuna Inu, Mbuyanga

ONE THING I FOR THE LORD

ONE THING I FOR THE LORD

1. Ndifuna Inu, Mbuyanga, Chifukwa ndagwa mthopemo,
Ndi madzi pena motowo, M’nditsuke ’ne, mnditsuke ’ne.

* CHORUS:
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Achoketu mu mtimanga.
*

2. Mukatsegula masowa, Ndidzakuyamikani ’Nu.
Komabe Mtima woyera, Udzapambana zonsezo.

3. Ukatsukidwa mtimawo Adzatseguka masowo.
Chifukwa kuti mwa Inu, Ndionamo za mmwambamo.

4. Ndayesa kudzikonzatu, Kuchotsa tchimo langalo
Ngakhale ndayesetsatu, Zoipazo zilipobe.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 54

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndifuna Inu, Mbuyanga as Hymn 54 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.