Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
62. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu
MY JESUS, I LOVE THEE
MY JESUS, I LOVE THEE
1. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu,
Ndisiya zoipa chifukwa chanu;
Ambuye wabwino ndi Mplumutsiyo;
Ndikonda tsopano koposa kale.
2. Ndikonda chifukwa munakonda ’ne;
Mnafera pa mtengo kuombola ’ne;
Mukhululukira zoipa zonse;
Ndikonda tsopano koposa kale.
3. Ndidzakukondani kosalekai,
Ndidzakutamani masiku onse.
Mpakatu ndidzafa ndidzanenabe,
Ndikonda tsopano koposa kale.
4. Ku malo owalo kumwamba komwe
Ndidzakuongani, Ambuye Yesu;
Ntavala korona ndizayimbabe,
Ndikonda tsopano koposa kale.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 62
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu as Hymn 62 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.