Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

68. Ndikonda Kunena Ndaomboledwa

REDEEMED! HOW I LOVE TO PROCLAIM IT

REDEEMED! HOW I LOVE TO PROCLAIM IT

1. Ndikonda kunena chifukwa, Ndaomboledwa ndi mwazi!
Ndaomboledwa mwa chifundo, Ndine wake nthawi zonse.*
*

*CHORUS:
Ndi mwazitu (ndi mwazitu) wa Yesu, ndaomboledwa;
Ndine wake (ndine wake) kosatha, ndaomboledwa.*

2. Ndinetu wokondwa mwa Yesu, Kukondwa kosaneneka;
Ndziwa kuti kuwala kwake Kumakhalabe ndi ine.

3. Ndisinkha za Mombolo wanga, Tsiku lonse ndisinkha ’Ye,
Ndiyimba wosakhala chete, Ndiyimba chikondi chake.

4. Ndidziwa kuti ndzamuona, Mfumu amene ndimkonda;
Yemwe amanditsogolera, Ndi kundisunga usiku.

5. Korona ali kudikira, Mmalo anga owalawo;
Msanga ndi oyera mtimawo Ndidzakhala ndi Ambuye.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 68

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndikonda Kunena Ndaomboledwa as Hymn 68 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.