Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
8. Pakwitana Mbuye Wanga
WHEN THE TRUMPET
WHEN THE TRUMPET
1. Pakwitana Mbuye wanga potsiriza dzikoli,
Pakufika tsiku la kuwalalo,
Posonkhana akumvera, pakuona Yesuyo,
Ndidzakondwerera naye komweko
*CHORUS:
Pakwitana Mbuye wanga (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wanga (Mbuyanga),
Pakwitana Mbuye wanga,
Ndidzakondwerera naye komweko.
*
2. Potuluka mmanda mwao, anthu ake onsewo,
Tidzasanganatu nao nthawiyo.
Pakuuka osankhidwa, kunka naye Yesuyo,
Ndidzakondwerera naye komweko.
3. Tisaleke kugwirabe ntchito ya Mulunguyo,
Tibukitse mbiri yake mdzikoli,
Ndi podzatha moyo wathu ndi zintchito zathuzo,
Tidzakondwerera naye komweko.
*CHORUS (lotsiriza):
Pakwitana Mbuye wathu (Mbuyathu),
Pakwitana Mbuye wathu (Mbuyathu),
Pakwitana Mbuye wathu,
Tidzakondwerera naye komweko.*
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 8
Permanent page: number and title URL
This page preserves Pakwitana Mbuye Wanga as Hymn 8 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.