Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

80. Tinke Ife Ku Ntchito Ya Mulungu

TO THE WORK!

TO THE WORK!

1. Tinke ife ku ntchito ya Ambuye;
Tizitsata mapazi a Mbuye Yesu.
Mau ake adzapatsa mphamvu yake,
Ndipo ndi mtima wonse tigwire ntchito.*
*

*CHORUS:
Gwirani ntchitoyo, Gwirani ntchitoyo,
Mpakatu Yesuyo, Adzabweranso mdzikoli.*

2. Tinke ife ku ntchito ya Mlungu wathu,
Yakudyetsa, Kumwetsa osowa onse.
Ndi mbendela ya mtanda tidzayendatu,
Pakulalika chipulumutso chake.

3. Tinke ife ku ntchito ya Mlungu wathu,
Ntchito ya kuchenjeza ilipo lero;
Ndi kwa anthu a mdima a mdziko lino,
Ndi kukweza Ambuye Ndi Mfumu yathu.

4. Tichitebe ntchito za Mlungu wathu,
Posachedwa Ambuye adzabweranso;
Ndipo ife tidzanka kumwamba naye,
Nyimbo zathu zokoma tidzayimbabe.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 80

Permanent page: number and title URL

This page preserves Tinke Ife Ku Ntchito Ya Mulungu as Hymn 80 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.