Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

85. Ndiyimba Mphamvu Ya Mulungu

I SING THE MIGHTY POWER

I SING THE MIGHTY POWER

1. Ndiyimba mphamvu ya Mlungu, wolenga mapiri,
Yemwe anapanga zinyanja ndi mlengalenga;
Ndiyimba nzeru imene inapanga dzuwa;
Mwezi uwala usiku, ndi nyenyezi zomwe.

2. Ndiyimba ubwino wake, Wakupatsa kudya;
Analenga zonse ndi mau, nayamikira.
Mbuye munazikhazika mozizwitsa ndithu!
Zinthu za m’dziko lapansi ndi zam’mbwamba zomwe.

3. Mbeu ndi maluwa omwe, zidziwitsa Inu;
Mitambo yonse ndi namondwe, zimvera Inu.
Za moyo zonse zimasamalidwa ndi Inu,
Tilibe kothawira’ko, koma kwanu kokha.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 85

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndiyimba Mphamvu Ya Mulungu as Hymn 85 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.