Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

95. Mulungu Watisunga ’Fe

SAFELY THROUGH ANOTHER WEEK

SAFELY THROUGH ANOTHER WEEK

1. Mlungu watisunga ’fe Mpaka mlungu winawu;
T’yeni timpembedze ’Ye, Tsiku lopumulali;
Tiganize zinthu za Mau a Mulunguyo.
Tiganize zinthu za Mau a Mulunguyo.

2. Pakufuna nsisizo, Zakudzera m’dzinalo,
Mudze, Mbuye wathu ’Nu, Mukhululukire ’fe;
Pakupuma mwanumo, Tikumbuka Inuyo.
Pakupuma mwanumo, Tikumbuka inuyo.

3. Pakulemekeza ’Nu, Tikuyandikira ’Nu;
Tikuona mphamvuyo, Ndi ulemelerowo.
Mtithangate Mbuyathu Kudya phwando m’mwambamo.
Mtithangate Mbuyathu Kudya phwando m’mwambamo.

4. Mbuye mugonjetsetu Tchimo la mu mtimanga,
Kuti ndikagwiretu Ntchito zokondwetsa ’Nu.
Masabata onsewo Alingane momwemo,
Masabata onsewo Alingane momwemo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 95

Permanent page: number and title URL

This page preserves Mulungu Watisunga ’Fe as Hymn 95 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.