Christ in Song Christ in Song Tumbuka

Nyimbo za Mpingo wa SDA · Christ in Song Tumbuka

124. Yesu Pera Wakwezgeke

### 124 Yesu Pera Wakwezgeke
NOT I, BUT CHRIST

1.
Ndikweze Yesu yekha m'zinthu zonse;
Amveke, aoneke yekhayo;
Mu ntchito, m'maganizo ndipo m'mau,
Ambuye aoneke yekhayo.

2.
Ndi Yesu atonthoza akulira,
Yekhayo angachotse msoziwo;
Yekhayo angatule akatundu,
Yekhayo angachotse manthawo.

3.
Ndileke mau onse ena chabe,
Ndileke zakupusa zangazo;
Ndikweze Yesu, ndisanyade konse,
Ndisadzitame, koma lyeyo.

4.
Ndi Khristu amapatsa 'ne zosowa.
Ndi yekha amapatsa mphamvunso.
Yekhayo m'thupi, m'moyo, ndi mu mzimu
Ndi Khristu yekha nthawi zonsezo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Nyimbo za Mpingo wa SDA

Search name: Christ in Song Tumbuka

Language: Tumbuka

Hymn number: 124

Permanent page: number and title URL

This page preserves Yesu Pera Wakwezgeke as Hymn 124 in Nyimbo za Mpingo wa SDA. It is part of the Christ in Song Tumbuka collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.