Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

130. Ndine Wanuyo

I AM THINE, O LORD

I AM THINE, O LORD

1. Ndine wanuyo, ndamva mauwo,
A chikondi chanucho;
Mundikoketu mfupi ndinuyo,
Mwa chikhulupirocho.

*CHORUS:
Mndisendeze (mfupi), mfupi mbuyanga,
Ndi pa mtanda wanuwo;
Mndisendeze mfupi, Mbuye wanga ’Nu,
Ndi pa mwazi wanuwo.*

2. M’ntchito yanu mndipatulire ’ne,
Mwa chisomo chanucho;
Moyo wangawo uyang’ane ’Nu,
Ndichitetu zanuzo.

3. Ndikondwera ’ne pakupitatu,
Kugwadira Mbuyeyo;
Pakunenatu naye mserimo,
Monga bwenzi langalo.

4. Sindidziwatu za chikondicho,
Mpaka n’dzanke tsidyalo;
Sindifikira za chimwemwecho,
Mpaka n’dzanke kwanuko.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 130

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndine Wanuyo as Hymn 130 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.