Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
131. Inetu Ndifunadi
MORE LIKE JESUS
MORE LIKE JESUS
1. Inetu ndifunadi Kufanana ndi Yesu,
Andidzaze mtimamo Ndi kufatsa kwakeko;
Ndidziyenda monga ’Ye Mdziko la zoipali;
Ndine wosaukadi, Yesu mkhale mtimanga.
2. Ngati amva khwangwala, Nayang’ana mphetazo,
Nasamala zonsezo, Ndithu andimveranso.
Adzandiphunzitsa ’ne, Nakhulukira ’ne;
Ndikhaletu wangwiro, Yesu mkhale mtimanga.
3. Popemphera ndikhale Monga Yesu Mbuyeyo;
Ndipumule mwa Iye, Andimwetse madziwo.
Mwa chisomo ndabadwa, Ndafa mwa zoipazo,
Ndikhulupiliretu, Yesu mkhale m’mtimanga.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 131
Permanent page: number and title URL
This page preserves Inetu Ndifunadi as Hymn 131 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.