Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
168. Yehova Ndi M’busa Wanga
THE LORD IS MY SHEPHERED
THE LORD IS MY SHEPHERED
1. Yehova ndi Mbusa, Sin’dzasowai,
Ndigona ku busa La msipu Wake
Anditsogolera Ku madzi ake,
Anditsitsimutsa Ndi mphamvu Yake.
2. Anditsogolera M’mabande mwake,
Chifukwa cha dzina Lokondedwalo.
Ngakhale ndiyenda Pafupi imfa,
Ha! sindidzaopa Zoipa zonse.
3. Chibonga ndi ndodo Za Mbusa wanga
Zindisangalatsa Masiku onse.
Mundiyalikira Pa maso panga,
Mkuona kwa mdani Chakudya changa.
4. Mudzoza mafuta Pa mutu panga,
Mwadzaza chifundo Mu chikho changa,
Udzanditsatira Ukoma wanu,
Ndidzakhala nanu Masiku onse.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 168
Permanent page: number and title URL
This page preserves Yehova Ndi M’busa Wanga as Hymn 168 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.