Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
169. Ugoneranjitu Mwana Wa Mfumu?
HEIR OF THE KINGDOM
HEIR OF THE KINGDOM
1. Ugoneranjitu mwana wa mfumu,
Kwinanso wayandikira m’mwamba?
Dzuka, nyamuka, uvale za nkhondo;
Bweratu nthawi isanathei.
2. Anthu a m’dziko adzanjenjemera,
Adzaopsedwa ndi kudza Kwake;
Mvetsa migugu abwera Ambuye,
Mwana wa mfumu usachedwatu.
3. Usachedwenso ndi zinthu za m’dziko,
Ulemerero udzathadi phe!
Dula zinsinga zolimba za m’dani,
Mwana wa mfumu kondwera ndithu.
4. Usayang’anetu kwina iyai,
Yembekezera ufumu wake;
Ona kuwala m’mapiri monsemo,
Mwana wa mfumu zileke zonse.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 169
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ugoneranjitu Mwana Wa Mfumu? as Hymn 169 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.