Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
217. Cinthu Cina Kwa Yesu
SOMETHING FOR JESUS
SOMETHING FOR JESUS
1. Mbuye! Cikondico ’natifera,
Cosandiyenera, ndidza kwanu;
Ndidziperekatu mphatso zanga zonse,
Sindidzamanatu cirri conse.
2. Wondipembedzera ndinu nokha
Ndiyembekezera pa Inutu;
Senzeni mtandawo ndiuze cikondi
Kuti ndingacite cinthu cina.
3. Zonse ndiri nazo nzolandira
Monga masikuwa’ kupita,
Ntchito yacikondi yayambidwa kale,
Otaika ena tikabweze.
4. Zonse ndiri nazo mwandipatsa,
Ndipatsa kwa Inu Ambuyanga
Nditafika m’mwamba moyo wanga ngwanu,
Cinthu cina nchanu nthawi zonse
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 217
Permanent page: number and title URL
This page preserves Cinthu Cina Kwa Yesu as Hymn 217 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.