Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
218. Maziko Amodzi
ONE FOUNDATION
ONE FOUNDATION
1. Maziko a mpingo amodzi ndi Kristu;
Colenga catsopano, mwa madzi ndi mau;
Anatsika kumwamba nalenga mpingowo;
Naugula ndi mwazi naufera mpingo.
2. Wokwanira mitundu yonse ya pa dziko;
Koma cipulumutso mwa njira imodzi,
Dzinali loyeretsa lapanga mpingowu,
Cogaawira cimodzi cisomo coyera.
3. Ponyoza mpingo wace anthu adzaona,
Adani apasula Thanthwe sadzalitha;
Oyerawo osunga cikhulupiriro;
Cisoni cikadzatha, tidzakondwerera.
4. M’kati mwa masauko a mpingo woyera;
Mpingo ulindirira cipulumutsoco;
Maso otopa nako kulira kukwera;
Mpingo waukuruwo udzagonjetsadi.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 218
Permanent page: number and title URL
This page preserves Maziko Amodzi as Hymn 218 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.