Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
230. Ndine Njira
I AM THE WAY
I AM THE WAY
1. Monga nkhosa zotayika, Zomwazika konse;
Zasiya moyo, mtendere, Njira yandisowa?
* CHORUS (Sop. & alto):
Ndine njira, co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa Ine,
Ndine njira, co’nadi, moyo,
Sungafike Atate komwa mwa Ine
(Bass and Tenor):
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moo
Sungafike Atate koma mwa ine,
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa ine.
*
2. Nkhawa zandisokoneza, Mulungu ndifuna;
Manena-nena ngambiri, Ndingagwire ziti?
3. Kwa Kristu, njira, co’nadi Ndi moyo ndibweranso;
Adzandifitsa kwa Tate, Kumalo kosatha.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 230
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ndine Njira as Hymn 230 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.