Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

231. Lowetsa Yesu Mu Mtima

LET JESUS COME INTO YOUR HEART

LET JESUS COME INTO YOUR HEART

1. Kodi watopa nazo zoipa, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati ufuna kutembenuka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

* CHORUS:
Leka kukayikatu; Usamkanenso lero,
Tsegula Mtima wako; Lowetsa Yesu mu Mtima.
*
2. Ukafuna kukhala woyera, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Madzi osamba ali pafupi, Lowetsa Yesu mu Mtima.

3. Ngati muli bvuto mtimamo, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati wapereweza za m’dziko, Lowetsa Yesu mu Mtima.

4. Abwenzi akakusandukira, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ndiye bwenzi losatekeseka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

5. Ngati uyimba nao odala, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Udzalowe m’nyumba za mpumulo, Lowetsa Yesu mu Mtima.

* CHORUS (wotsiriza):
Leka kukayikaku; Usamkanenso lero,
Ndatsegula citseko, Kuti Yesu alowemo.*

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 231

Permanent page: number and title URL

This page preserves Lowetsa Yesu Mu Mtima as Hymn 231 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.