Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

267. Fesa Mbeuu Za Cikondi

SCATTER SEEDS OF KINDNESS

SCATTER SEEDS OF KINDNESS

1. Tisonkhanitse zabwino, M’njira mwathu monsemo;
Tisunge tirigu yekha, Titaye zacabezo;
Tipeze zokondweretsa M’madalitso a lero,
Mwa cipiriro ticotse Minga yokhumudwitsa.

* CHORUS:
Ufese zacifundo, Ufese zacifundo
Ufese zacifundo, Zomwe tidzakolola
*
2. Sitisamala maluwa Ndi mbalame poyimba,
Mpaka mbalame ndiponso maluwa zitacoka;
Dzuwa sitisamala Pa nthawi ya cilimwe,
Akafikanso mazizi Nthaawiyo tilifuna.

3. Mwana akacita ngozi Poswa cikho comwera
Kodi mukalipa ko’psa Poturutsa tsinyalo?
Mukudziwa kuti mawa Adzakhala wakufa,
Kodi pakukwiya naye Mupsa Mtima leroli?

4. Poganizira za m’mbuyo Za zomwe tinacita,
Za mauwo okalipa Okhumutsidwa ena,
Ndi nchito zosaganiza; Izi zitikumbutsa
Kufetsatu zacifundo zomwe tidzakolola.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 267

Permanent page: number and title URL

This page preserves Fesa Mbeuu Za Cikondi as Hymn 267 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.