Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
268. Bata Ndu!
PEACE STILL
PEACE STILL
1. Mbuye, Nyanja yakalipa, Mafunde akweretsa!
Mlengalenga nawonso wada; Kodi tifere m’madzi;
Kodi simukusamala, Mugoneranjiko?
Pamene ife tiri ndi mantha, Kodi tifere m’madzi?
* CHORUS:
Namondweyo andimvera Ine, bata ndu! (Bata ndu!)
Ngakhale Nyanja zikalipe,
Ziwanda, anthu, ngakhale zinazo,
Madzi sangamize bwato Mwini
Nyanja ndi mtunda ali momwemo;
Zonse zingondimvera Ine; Batu ndu, bata ndu!
Zonse zingondimvera Ine; Batadi ndu!
*
2. Mbuye bvuto mu mtimamu Landibvuta leroli;
Kucirimika konse kwatha; Ndipulumutsenitu
Nkhwenkhwe ya chimo yozunza, Inditsirizitsa;
Ndamuka ine, ndamuka, Mbuye! Dzandipulumutseni.
3. Mbuye zobvutazo zatha, Kwagwa bata tsopano,
Kwawalal ngati kalirole, Ngati ndiri Kumwamba;
Msandisiyenso Ambuye, Tikhale Pamodzi;
Ndikafike ku gombe lodala, Mukandipumulitse.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 268
Permanent page: number and title URL
This page preserves Bata Ndu! as Hymn 268 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.