Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

274. Ndiri Ndi Mbuye

I HAVE A SAVIOUR

I HAVE A SAVIOUR

1. Ndiri ndi Mbuye wodandaulira,
Akonda Iyeyu kuposa dziko;
Pano andiyang’anira mwacifundo,
Ndifunatu akhale wa inunso!

* CHORUS:
Ndipempherera’nu, Ndipempherera’nu,
Ndipempherera’nu, Ndipempherera’nu,
*
2. Ndiri ndi Tate andipatsa ine
Ciyembekezo ca moyo wosatha;
Sacedwa kuitana tipite kwathu;
Ndifuna adzalandire inunso!

3. Ndiri n’zobvala, zopanda mabanga
Aindilindira mu ulemelero;
Wowalal monsemo konko ndizalandira,
Bwenzi ndifuna ukalandirenso!

4. Pamene Yesu wakupeza iwe,
Tauzatu ena za mtendererewo
Mwini ndiye Kristu yemweyo apatsa,
Mtendere ndifuna mulandirenso!

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 274

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndiri Ndi Mbuye as Hymn 274 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.