Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
275. Kosatha! N’kuti?
ETERNITY - WHERE
ETERNITY - WHERE
1. "Kosatha! - n’kuyi?" Ndilo funsolo;
Konse komwe uli liri komweko!
Udzakhala kuti nthawi zosatha!
Udzakhala kuti nthawi zosatha!
2. "Kosatha! N’kuti?" Kosatha n’kuti?
Ndi oomboledwa? Ndi otaika?
Mbali izi njiti - "Kosatha! N’kuti?"
Mbali izi njiti - "Kosatha! N’kuti?"
3. "Kosatha! N’kuti?" Uchitiranji
Zokondwa za dziko mosaganiza?
Popanda kusankha - "Kosatha! N’kuti?"
Popanda kusankha - "Kosatha n’kuti?
4. "Kosatha! N’kuti?" Bwenzi samala;
Adzaweruzatu Mulungu msanga
Lero linganene - "kosatha! N’kuti?"
Lero linganene - "Kosatha! N’kuti?
5. "Kosatha! N’kuti?" Kosatha! N’kuti?"
Bwenzi usagone, lekana m’dziko,
Mpaka utayankha - "Kosatha! N’kuti?"
Mpaka utayankha - "Kosatha! N ’kuti.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 275
Permanent page: number and title URL
This page preserves Kosatha! N’kuti? as Hymn 275 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.