Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

28. Khalatu Woyera

TAKE TIME TO BE HOLY

TAKE TIME TO BE HOLY

1. Khalatu woyera, Pemphera mseri;
Werenga mau ’ke, Masiku onse;
Thangatani omwe Ali ofo’ka,
Madalitso ake Funafunani.

2. Khalatu woyera, Dziko laipa;
Pemphera kolimba, Kwa Yesu Mbuye;
Yang’anitsa Yesu, Ndi Kumtsatira
Kuti anthu ena Aone Yesu.

3. Khalatu woyera, Akutsogoze,
Usamtsogolere, M’njira zakozo;
M’nsoni ndi pokondwa, Tsata Mbuyako
Khulupira Yesu Ndi mau ake.

4. Khalatu woyera, Khala wofatsa,
Alamulire ’Ye, Ganizo lako;
Utatsogozedwa Ndi Mzimu wake,
Msanga udzagwira Ntchito ya mmwamba.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 28

Permanent page: number and title URL

This page preserves Khalatu Woyera as Hymn 28 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.