Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
29. Mukhale Ndine
ABIDE WITH ME
ABIDE WITH ME
1. Mukhale ndine dzuwa lalowa, Wagwa usiku bwenzi lisowa,
Ndilibe wina wondithandiza, Wa mphamvu ndinu, mkhale ndinetu.
2. Kamoyo kanga katha leroli, Zidzachokanso zinthu za dziko,
Zimasinthika zoonekazo, Simusinthika mkhale ndinetu.
3. Koma kale mnakhalitsa pano, Mukhale ndine musachokenso,
Simpempha kuti Mbuye mutsotse, Komatu mukhalitse ndinetu.
4. Ndifuna inu tsiku lonselo, Ndi mphamvu yanu ndidzasungika,
Mukatsogola sindiopai, Msana, usiku, mkhale ndinetu.
5. Adani sindiopa mulipo, Muletse tsoka ndi chisonichi,
Ikadza imfa ndzalimba mtima, M’imfa ndi moyo mkhale ndinetu.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 29
Permanent page: number and title URL
This page preserves Mukhale Ndine as Hymn 29 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.