Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

281. Nyenyezi Yabwino

A BEAUTIFUL STAR

A BEAUTIFUL STAR

1. Nyenyezi yabwino yowala ndi ulemerero wa m’mwamba
Kuwala kwace kotsogoza anzeru napeza mwana

* CHORUS:
Yowalayo, yowalayo, Nyenyezi yabwino m’phiri,
Yowalayo, yowalayo, Cipulumutso ca Mlungu.
*
2. Mau anawadziwitsadi nthawi yafika ya nyenyezi,
Anaitsata yowalayo – Ndi "Kristu nthanda ya m’mawa"

3. Nafe titsate monga iwo, Muni wa dziko wonenedwa’
Titsate monga iwo, Muni wa dziko wonenedwa;
Titsate mpaka tikafike, Ku Mpumula wa kumwamba.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 281

Permanent page: number and title URL

This page preserves Nyenyezi Yabwino as Hymn 281 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.