Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

301. Ambuye Ali Pafupi Kudza

’TIS ALOMOST TIME FOR THE LORD TO COME

’TIS ALOMOST TIME FOR THE LORD TO COME

1. Ambuye ali pafupi kudza, Ndikumvaconcodi,
Ndiponso nyenyezi zikuzima, Tsopano ndi mbanda kucatu

* CHORUS:
Ee! Tsopano ndi mbanda kucatu!
Ee! Tsopano ndi mbanda kuca ndithu!
Usiku wathadi! Usana wadzanso.
Ee! Tsopano ndi mbanda kucatu!

* 2. Zizindikiro za mlengalenga Zilalikiradi;
Ndi za pa dziko zinena kuti Ambuye wayandikira

3. Ndi nthawi yoti kunyada kuthu Mu mpingo wonsewo;
Ukhale wofulumira ntchito, Ukhale woyang’aniratu

4. Pitani msanga kukalalika Kwa osaukawo;
Ndi kwa omveka a dziko lino; Onsewo afulumirenso.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 301

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ambuye Ali Pafupi Kudza as Hymn 301 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.