Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

302. Mulungu Wa Kumwamba

(Upon Dedicating a Church)

(Upon Dedicating a Church)

1. Mulungu wa kumwamba, tabwera kunoku,
Ndi Mtima wokondwera kulowa m’nyumbayi
Cifukwa ca zabwino mwacitazi
Titokuyamikirani leroli.

* CHORUS:
Inde tikuyamikani, Atate, leroli,
Mwatimangira ’fe kuno kacisi wanuyu!
Ndi ulemerero wanu mudzadze m’mnyumbayi;
Muyeretse, mudalitse, munomu
*
2. Tikondwa tonse kukuthokozani ’Nu
Poyamba kupemphera ndi kuyimbiramu
Mom’muno nsiku zonse mukhale nafetu
Monga nd angelo anu m’mwambamo.

3. Ikhale ngati nyali, yowala m’nyumbayi,
Yakutsogoza onse opunthwa m’mdima bii,
Akunja ndi Akhristu mwapulumutse ndi kuunika koturuka munomu.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 302

Permanent page: number and title URL

This page preserves Mulungu Wa Kumwamba as Hymn 302 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.