Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
37. Ndidze Pafupipa
NEARER MY GOD TO THEE!
NEARER MY GOD TO THEE!
1. Ndidze pafupipa Mlungu wanga,
’Ngakhale ndi tsoka Mundibweza,
Koma ndiyimbabe, Mbuye m’ndikhalitse
Mbuye m’ndikhalitse, M’fupi Ndinu.
2. Ngakhale ku thengo, Ndasochera,
M’mdima ndigonapo, E pa mwala.
Koma m’kulotako, Ndiyandikizanso.
Ndiyandikizanso, M’fupi Ndinu.
3. Pajapo ndipenya Pokwerapo,
Angelo atsika Kumwambako,
Ndiwo akodola Kuti ndibwerere,
Kuti ndibwerere, M’fupi Ndinu.
4. Tsono poukanso Wokondwatu,
Ndipeza pomwepo Pali Mlungu;
Ndipo masautso Andisendezanso,
Andisendezanso, M’fupi Ndinu.
5. Podzabwera Iye N’dzanka naye,
Dzuwa ndi nyenyezi Zitsalira;
Pomwe ndiyimbanso, Ndidza pafupipo,
Ndidza pafupipo, Mlungu wanga.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 37
Permanent page: number and title URL
This page preserves Ndidze Pafupipa as Hymn 37 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.