Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa
41. Mulungu Akhala Ndi Inu
GOD BE WITH YOU!
GOD BE WITH YOU!
1. Mulungu akhale ndi inu, Mpaka tidzaonananso;
Atsogoze, asunge ’nu; Mulungu akhale ndi inu.
*CHORUS:
Asunga nonsenu, Tikomana ndi Yesu,
Asunga nonsenu, Mulungu akhale ndi inu.*
2. Mulungu akhale ndi inu, Ndi mapiko akubisa,
Masiku onse kudyetsa; Mulungu akhale ndi inu.
3. Mulungu akhale ndi inu, Ndi pamene muvutika,
Adzakuthangatani ’nu, Mulungu akhale ndi inu.
4. Mulungu akhale ndi inu, Ndi chikondi chake chonse,
Asunge mzoopsya zonse, Mulungu akhale ndi inu.
Help keep these hymns free
Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.
♥ DonateHymn details
Hymnal: Khristu Mu Nyimbo
Search name: Christ in Song Chichewa
Language: Chichewa
Hymn number: 41
Permanent page: number and title URL
This page preserves Mulungu Akhala Ndi Inu as Hymn 41 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.
Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.
Reading and preservation note
Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.