Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

40. Poyenda Ndi Mbuye

TRUST AND OBEY

TRUST AND OBEY

1. Poyenda ndi Mbuye, mkuwala kwakeko, Aunikira m’njira mwathu;
Pakugwira ntchito amakhala nafe, Ndi onse amene amvera.

*CHORUS:
Khulupira, palibenso njira, Yakukondwa mwa Yesu,
Komatu kumvera.

*2. Mthunzi sungagwetu, pena mtambo mmwamba, Komatu azipirikitsa;
Nkhawa ndi chisoni zidzachoka ngati, Tikhulupira ndi kumvera.

3. Chifukwa cha ntchito ndi zisoni zathu, Adzatilipira mokwana;
Kopandanso imfa, kapena kukwiya, Tidzadalitsika pomvera.

4. Sitingadziwetu zachikondi chake, Mpaka titadziperekatu;
Chifukwa chifundo ndi chimwemwe chake, Amapatsa anthu omvera.

5. Pompo m’chiyanjano tidzakhala naye, Kapena kuyenda ndi Iye;
Ndipo tidzachita chifuniro chake, Tidzakhala omvera ndithu.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 40

Permanent page: number and title URL

This page preserves Poyenda Ndi Mbuye as Hymn 40 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.