Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

44. Ndidzamdziwa Mombolo Wanga

WHEN MY LIFE-WORK IS ENDED

WHEN MY LIFE-WORK IS ENDED

1. Pamene nditatha zintchito zanga zonsezo,
Nditaoloka pa tsidya la nyanja;
Chakufachi chikadzavalatu chosafanso;
Pompo ndidzamdziwa Mombolo wanga.

*CHORUS:
Ndidzamdziwa, Ndidzamdziwa, Podzaima pa mbali pakepo,
Ndidzamdziwa, ndidzamdziwa, Ndi misomali m’manja mwake.

*2. Moyo wanga udzakondwera pakumuona,
Ndi kuona nkhope yake yowala;
Ndidzamyamika Iye ndi mtima wanga wonse,
Malo adandikonzera kumwamba.

3. Ee! ndidzakondwa pakuona okondedwawo
Omwe ndalekana nawo m’dzikoli;
Koma n’dzayamba ndaonana naye Yesuyo,
Wokondedwa wanga wopambanayo.

4. Kupyolera pa zipata kunka ku mzindawo,
Iye adzanditsogolera ine,
Nyimbo ya nthawi zonse ndidzayimba mokondwa;
Nditamuona Mpulumutsi wanga.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 44

Permanent page: number and title URL

This page preserves Ndidzamdziwa Mombolo Wanga as Hymn 44 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.