Christ in Song Christ in Song Chichewa

Khristu Mu Nyimbo · Christ in Song Chichewa

45. Patseni Bible

GIVE ME THE BIBLE

GIVE ME THE BIBLE

1. Patseni Bible ndilo ndikufuna, Ndi chotitsogolera njirayo;
Monga mapiri oonetsa kwathu, Obweza anthu osocherawo.

*CHORUS:
Patseni Bible ndilo mau ake, Mau oyera a Mulunguyo,
Ndilo pangano la chikondi chake, ndi nyali mnjira yonka m’mwambamo.

*2. Patseni Bible ndilo ndikufuna, Mmene usweka mtima wangawo;
Patseni mau a Ambuye Yesu, Mau okondweretsa mmtimanga.

3. Patseni Bible ndilo ndikufuna, Nyali ya kusonyeza njirayo,
Mmene ndingagwe lindipulumutsa, Lindisonyeza tchimo langalo.

4. Patseni Bible ndilo ndikufuna, Liunikira a mu mdimawo,
Ndilo chiyembekezo kwa olira, Ndi nyali m’njira yonka m’mwambamo.

Help keep these hymns free

Your donation can help maintain the website, improve accessibility and keep the hymns freely available.

Hymn details

Hymnal: Khristu Mu Nyimbo

Search name: Christ in Song Chichewa

Language: Chichewa

Hymn number: 45

Permanent page: number and title URL

This page preserves Patseni Bible as Hymn 45 in Khristu Mu Nyimbo. It is part of the Christ in Song Chichewa collection within a multilingual Adventist hymn archive built for reading, searching, sharing and comparing hymn traditions across languages.

Use the previous and next buttons to continue through this hymnal, or return to the collection page to search by number and title. The reading tools above let you adjust text size, save favourites and share the hymn with others.

Reading and preservation note

Historic and regional hymn texts can contain spelling differences, older punctuation, local wording and transcription variations. This archive keeps the hymns searchable while allowing future corrections and improvements to be made carefully.